19 Ndipo poyenda zamoyozo, njingazi zinayenda pambali pao; ndipo ponyamuka pansi zamoyozo, njinga zinanyamuka.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:19 nkhani