20 Kuli konse mzimu ukuti umuke, zinamuka komwe mzimu ukuti umuke; ndi njingazi zinanyamuka pambali pa izo; pakuti mzimu wa zamoyozo unali m'njingazo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:20 nkhani