21 Poyenda zija zinayenda izi, poima zija zinaima izi; ndipo ponyamuka pansi zija njingazi zinanyamuka pambali pa izo; pakuti mzimu wa zamoyozo unali mu njingazi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:21 nkhani