22 Ndi pa mitu ya zamoyozi panali cifaniziro ca thambo, monga mawalidwe a krustalo woopsa, loyalika pamwamba pamitu pao.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:22 nkhani