23 Ndi pansi pa thambolo mapiko ao analunjikana, lina kulunjika ku linzace; ciri conse cinali nao mapiko awiri akuphimba matupi ao, cakuno ndi cauko.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:23 nkhani