8 Zinali naonso manja a munthu pansi pa mapiko ao pa mbali zao zinai; ndipo zinaizi zinali nazo nkhope zao ndi mapiko ao.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 1
Onani Ezekieli 1:8 nkhani