Ezekieli 10:21 BL92

21 Yense anali nazo nkhope zinai, ndi yense mapiko anai, ndi cifaniziro ca manja a munthu pansi pa mapiko ao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 10

Onani Ezekieli 10:21 nkhani