22 Ndi cifaniziro ca nkhope zao ndico nkhope zomwezo ndinaziona kumtsinje Kebara, maonekedwe ao ndi iwo eni; ali yense anayenda, nalunjika m'tsogolo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 10
Onani Ezekieli 10:22 nkhani