Ezekieli 10:4 BL92

4 Ndipo ulemerero wa Yehova unakwera kucokera kukerubi kumka ku ciundo ca nyumba; ndi nyumba inadzala nao mtambo, ndi bwalo linadzala ndi ceza ca ulemerero wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 10

Onani Ezekieli 10:4 nkhani