5 Ndipo mkokomo wa mapiko a akerubi unamveka mpaka bwalo lakunja, ngati mau a Mulungu Wamphamvuyonse, pakunena Iye.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 10
Onani Ezekieli 10:5 nkhani