Ezekieli 11:11 BL92

11 Mudzi uno sudzakhala mphika wanu, ndi inu simudzakhala nyama m'kati mwace, ndidzakuweruzirani ku malire a Israyeli;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11

Onani Ezekieli 11:11 nkhani