Ezekieli 11:12 BL92

12 ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakuti simunayenda m'malemba anga, kapena kucita maweruzo anga, koma mwacita monga mwa maweruzo a amitundu okhala pozungulira panu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11

Onani Ezekieli 11:12 nkhani