19 Ndipo ndidzawapatsa mtima umodzi, ndi kuika mzimu watsopano m'kati mwao; ndipo ndidzawacotsera mtima wamwala m'thupi mwao, ndi kuwapatsa mtima wamnofu;
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11
Onani Ezekieli 11:19 nkhani