20 kuti ayende m'malemba anga, ndi kusunga maweruzo anga, ndi kuwacita; ndipo adzakhala anthu anga, ndi Ine ndidzakhala Mulungu wao.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11
Onani Ezekieli 11:20 nkhani