Ezekieli 12:22 BL92

22 Wobadwa ndi munthu iwe, ngwotani mwambi umene muli nao m'dziko la Israyeli, wakuti, Masiku acuruka, ndi masomphenya ali onse apita pacabe?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:22 nkhani