Ezekieli 12:23 BL92

23 Cifukwa cace unene nao, Atero Yehova Mulungu, Ndidzaleketsa mwambi uwu, ndipo sadzauchulanso mwambi m'Israyeli; koma unene nao, Masiku ayandikira, nadzacitika masomphenya ali onse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:23 nkhani