Ezekieli 13:17 BL92

17 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, uziika nkhope yako itsutsane nao ana akazi a anthu ako, akunenera za m'mtima mwao, nunenere cowatsutsa,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:17 nkhani