Ezekieli 13:6 BL92

6 Iwo aona zopanda pace, ndi phenda labodza amene anena, Atero Yehova; koma Yehova sanawatuma, nayembekezetsa anthu kuti mauwo adzakhazikika.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:6 nkhani