Ezekieli 13:5 BL92

5 Simunakwera kuima mopasuka, kapena kumanganso linga la nyumba ya Israyeli, kuima kunkhondo tsiku la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:5 nkhani