Ezekieli 15:6 BL92

6 Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Ngati mtengo wampesa pakati pa mitengo ya kunkhalango ndauponya kumoto ukhale nkhuni, momwemo ndidzapereka okhala m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 15

Onani Ezekieli 15:6 nkhani