7 Ndipo ndidzaika nkhope yanga iwatsutse; adzaturuka kumoto, koma moto udzawatha; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakuika Ine nkhope yanga iwatsutse.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 15
Onani Ezekieli 15:7 nkhani