Ezekieli 16:10 BL92

10 Ndinakubvekanso ndi nsaru zopikapika, ndi kukubveka nsapato za cikopa ca katumbu; ndinakuzenenga nsaru yabafuta, ndi kukuphimba ndi nsaru yasilika.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16

Onani Ezekieli 16:10 nkhani