15 Koma unatama kukongola kwako, ndi kucita zacigololo potama mbiri yako, ndi kutsanulira zigololo zako pa munthu ali yense wopitapo; unali wace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16
Onani Ezekieli 16:15 nkhani