44 Taona, ali yense wonena miyambi adzakunenera mwambi uwu, wakuti, Monga mace momwemo mwana wace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16
Onani Ezekieli 16:44 nkhani