Ezekieli 17:19 BL92

19 Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Pali Ine, lumbiro langa, analipepula, ndi pangano langa analityola, ndidzawabweza pamutu pace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17

Onani Ezekieli 17:19 nkhani