Ezekieli 17:20 BL92

20 Ndidzamphimbanso ndi ukonde wanga, nadzakodwa iye mu msampha wanga; ndipo ndidzadza naye ku Babulo, ndi kunena naye komweko mlandu wa kulakwa kwace anandilakwira nako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17

Onani Ezekieli 17:20 nkhani