Ezekieli 17:21 BL92

21 Ndipo othawa ace onse m'magulu ace onse adzagwa ndi lupanga, ndi otsala adzabalalitsidwa ku mphepo zonse; ndipo mudzadziwa kuti Ine Yehova ndanena.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17

Onani Ezekieli 17:21 nkhani