22 Atero Ambuye Yehova, Ndidzatenganso nsonga ya mkungudza wautali ndi kulika; ndidzabudula nsonga yosomphoka'ya nthambi zace zanthete, ndi kuioka pa phiri lalitali lothubvuka;
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17
Onani Ezekieli 17:22 nkhani