3 nuziti, Atero Ambuye Yehova, Ciombankhanga cacikuru ndi mapiko akuru, ndi maphiphi atali, odzala nthenga ca mathotho-mathotho, cinafika ku Lebano, nicitenga nsonga ya mkungudza,
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17
Onani Ezekieli 17:3 nkhani