Ezekieli 17:5 BL92

5 Cinatengakonso mbeu ya m'dziko, ndi kuibzala m'nthaka yokoma, cinaiika panali madzi ambiri, cinaioka ngati mtengo wamsondodzi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17

Onani Ezekieli 17:5 nkhani