Ezekieli 17:6 BL92

6 Ndipo inaphuka, nikhala mpesa wotambalala wofupi msinkhu, nthambi zace zinapindikira momwe, ndi mizu yace pansi pace, nikhala mpesa, nuonetsa nthambi ndi kuphuka mphukira.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17

Onani Ezekieli 17:6 nkhani