25 Koma mukuti, Njira ya Ambuye njosayenera. Tamvera tsono nyumba ya Israyeli, Kodi njira yanga njosayenera? njira zanu si ndizo zosayenera?
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18
Onani Ezekieli 18:25 nkhani