7 wosasautsa munthu ali yense, koma wambwezera wangongole cigwiriro cace, wosatenga zofunkha, anampatsa wanjala cakudya cace, nabveka wamarisece ndi cobvala,
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18
Onani Ezekieli 18:7 nkhani