Ezekieli 19:14 BL92

14 Unaturukanso moto ku ndodo za ku nthambi zace, unatha zipatso zace; m'mwemo ulibe ndodo yolimba ikhale ndodo yacifumu ya kucita ufumu. Iyi ndi nyimbo idzakhala nyimbo ya maliro.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 19

Onani Ezekieli 19:14 nkhani