Ezekieli 20:1 BL92

1 Ndipo kunali caka cacisanu ndi ciwiri, mwezi wacisanu; tsiku lakhumi la mwezi, anadza akulu ena a Israyeli kufunsira kwa Yehova, nakhala pansi iwowa pamaso panga.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:1 nkhani