Ezekieli 19:8 BL92

8 Pamenepo mitundu ya anthu inadzipereka kuukola kucokera ku maiko a ku mbali zonse, niuphimba ndi ukonde wao, nugwidwa uwu m'mbuna mwao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 19

Onani Ezekieli 19:8 nkhani