Ezekieli 19:7 BL92

7 Ndipo unadziwa amasiye ao, nupasula midzi yao, ndipo dziko ndi kudzala kwace linasanduka labwinja, cifukwa ca phokoso la kubangula kwace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 19

Onani Ezekieli 19:7 nkhani