Ezekieli 20:38 BL92

38 ndipo ndidzasankhula mwa inu opanduka ndi ondilakwira, ndidzawaturutsa m'dziko logoneramo iwo; koma sadzalowa m'dziko la Israyeli; motero mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:38 nkhani