Ezekieli 20:42 BL92

42 Ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakukulowetsani Ine m'dzil ko la Israyeli, m'dzikoli ndinalikwezera dzanja langa kulipereka kwa makolo anu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:42 nkhani