Ezekieli 20:46 BL92

46 Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako njira ya kumwera, nubenthulire mau kumwera, nunenere nkhalango ya kuthengo la kumwera kwa Yuda;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:46 nkhani