Ezekieli 20:6 BL92

6 tsiku lomwelo ndinawakwezera dzanja langa kuwaturutsa m'dziko la Aigupto, kumka nao ku dziko ndinawazondera, moyenda mkaka ndi uci, ndilo lokometsetsa mwa maiko onse;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 20

Onani Ezekieli 20:6 nkhani