Ezekieli 21:21 BL92

21 Pakuti mfumu ya ku Babulo aima pa mphambano ya njira, polekana njira ziwirizo, kuti aombeze maula; agwedeza mibvi, afunsira kwa aterafi, apenda ndi ciwindi.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21

Onani Ezekieli 21:21 nkhani