22 M'dzanja lace lamanja muli ula wa ku Yerusalemu, kuika zogundira, kutsegula pakamwa pa kupha, kukweza mau ndi kupfuula, kuikira zitseko zogundira, kuundira mtumbira, kumanga malinga.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21
Onani Ezekieli 21:22 nkhani