Ezekieli 21:23 BL92

23 Ndipo kudzakhala ngati kuombeza konyenga pamaso pa iwo amene anawalumbirira malumbiro; koma akumbutsa mphulupulu kuti akodwe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 21

Onani Ezekieli 21:23 nkhani