Ezekieli 22:3 BL92

3 Nuziti, Atero Ambuye Yehova, Ndiwo mudzi wokhetsa mwazi pakati pace, kuti nthawi yace ifike, nudzipangire mafano kudzidetsa nao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22

Onani Ezekieli 22:3 nkhani