Ezekieli 22:31 BL92

31 Cifukwa cace ndinawatsanulira ukali wanga, ndawatha ndi moto wa kuzaza kwanga, njira yao yao ndinaibweza pa mutu pao, ati Ambuye Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22

Onani Ezekieli 22:31 nkhani