Ezekieli 22:30 BL92

30 Ndipo ndinafunafuna munthu pakati pao wakumanganso linga, ndi kuimira dziko popasukira pamaso panga, kuti ndisaliononge; koma ndinapeza palibe.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 22

Onani Ezekieli 22:30 nkhani