15 omangira malamba m'cuuno mwao, ndi nduwira zazikuru zonika pamitu pao, maonekedwe ao ngati akalonga onsewo, akunga a ku Babulo, dziko la kubadwa kwao ndi Kasidi.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:15 nkhani