17 Namdzera a ku Babulo ku kama wa cikondi, namdetsa ndi cigololo cao, iyenso anadetsedwa nao; atatero moyo wace unafukidwa nao.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:17 nkhani