18 M'mwemo iye anaulula cigololo cace, nabvula umarisece wace; pamenepo moyo wanga unaipidwa naye, monga umo moyo unaipidwira mkuru wace.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 23
Onani Ezekieli 23:18 nkhani